Oweruza 11:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yefita anati kwa akuru a Gileadi, Mukaodifikitsanso kwathu kucita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkuru wanu kodi?

Oweruza 11

Oweruza 11:7-10