Oweruza 11:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Atate wanga, mwamtsegulira Yehova pakamwa panu, mundicitire ine monga umo mudaturutsa mau pakamwa panu; popeza Yehova anakucitirani inu cilango pa adani anu, pa ana a Amoni.

Oweruza 11

Oweruza 11:28-40