Oweruza 11:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yefita anathawa abale ace, nakhala m'dziko la Tobu; ndipo anyamata opanda pace anasonkhana kwa Yefita, naturuka naye pamodzi.

Oweruza 11

Oweruza 11:1-8