Nyimbo 8:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikadakutsogolera, kukulowetsa m'nyumba ya amai,Kuti andilange mwambo; Ndikadakumwetsa vinyo wokoleretsa,Ndi madzi a makangaza anga.

Nyimbo 8

Nyimbo 8:1-11