Nyimbo 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinagona tulo, koma mtima wanga unali maso:Ndi mau a bwenzi langa mnyamatayo agogoda, nati,Nditsegulire, mlongwanga, wokondedwa wanga, nkhunda yanga, wangwiro wanga:Pakuti pamtu panga padzala mame,Patsitsi panga pali madontho a usiku.

Nyimbo 5

Nyimbo 5:1-7