Nyimbo 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndalowa m'munda mwanga, mlongwanga, mkwatibwi:Ndachera nipa yanga ndi zonunkhiritsa zanga;Ndadya uci wanga ndi cisa cace;Ndamwa vinyo wanga ndi mkaka wanga.Idyani, atsamwalinu,Imwani, mwetsani cikondi.

Nyimbo 5

Nyimbo 5:1-5