Nyimbo 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'kamwa mwace muli mokoma: inde, ndiye wokondweretsa ndithu.Ameneyu ndi wokondedwa wanga, ameneyu ndi bwenzi langa,Ana akazi inu a ku Yerusalemu.

Nyimbo 5

Nyimbo 5:12-16