Ha, cikondi cako ncokongola, mlongwanga, mkwatibwi!Kodi cikondi cako siciposa vinyo?Kununkhira kwa mphoka yako ndi kuposa zonunkhiritsa za mitundu mitundu!