Numeri 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti aperekedwa konse kwa Ine ocokera mwa ana a Israyeli; ndadzitengera iwo m'malo mwa onse akutsegula m'mimba, ndiwo oyamba kubadwa a ana a Israyeli.

Numeri 8

Numeri 8:8-26