Numeri 8:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Momwemo upatule Alevi mwa ana a Israyeli; kuti Alevi akhale anga.

15. Ndipo atatero alowe Alevi kucita Debito ya cihema cokomanako; ndipo uwayeretse, ndi kuwapereka ngati nsembe yoweyula.

16. Pakuti aperekedwa konse kwa Ine ocokera mwa ana a Israyeli; ndadzitengera iwo m'malo mwa onse akutsegula m'mimba, ndiwo oyamba kubadwa a ana a Israyeli.

Numeri 8