Numeri 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akalonga a Israyeli, akuru a nyumba za makolo ao, anapereka nsembe, ndiwo akalonga a mapfuko akuyang'anira owerengedwa;

Numeri 7

Numeri 7:1-12