Numeri 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Uza ana a Israyeli kuti aziturutsa m'cigono akhate onse, ndi onse akukhala