Numeri 4:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anawawerenga monga mwa mau a Yehova ndi dzanja la Mose, onse monga mwa nchito zao, ndi monga mwa akatundu ao; anawawerenga monga momwe Yehova adauza Mose.

Numeri 4

Numeri 4:40-49