Numeri 26:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Rubeni, ndiye woyamba kubadwa wa Israyeli; ana amuna a Rubeni ndiwo: Hanoki, ndiye kholo la banja la Ahanoki; Palu, ndiye kholo la banja la Apalu;

Numeri 26

Numeri 26:1-12