Numeri 26:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awawerenge kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu; monga Yehova anawauza Mose ndi ana a Israyeli, amene adaturuka m'dziko la Aigupto.

Numeri 26

Numeri 26:1-7