Numeri 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

natsata munthu M-israyeli m'hema, nawamoza onse awiri, munthu M-israyeli ndi mkaziyo m'mimba mwace. Pamenepo mliri unaletseka kwa ana a Israyeli.

Numeri 25

Numeri 25:1-11