Numeri 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Pinehasi mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni wansembe, anaciona, anauka pakati pa khamu, natenga nthungo m'dzanja lace;

Numeri 25

Numeri 25:2-15