Numeri 22:39-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Ndipo Balamu anamuka ndi Balaki, nafika iwo ku Kiriyati Huzoti.

40. Pamenepo Balaki anapha ng'ombe ndi nkhosa, natumizira Balamu, ndi akalonga okhala naye.

41. Ndipo kunali kuti m'mawa, Balaki anatenga Balamu, nakwera nave ku misanje ya Baala, ndi kumeneko anaona malekezero a anthuwo.

Numeri 22