Numeri 23:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Ndimangireni kuno maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere kuno ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.

Numeri 23

Numeri 23:1-6