Numeri 2:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anacita monga mwa zonse Yehova adauza Mose, momwemo anamanga mahema ao pa mbendera zao, momwemonso anayenda paulendo, yense monga mwa mabanja ace, monga mwa nyumba za makolo ace.

Numeri 2

Numeri 2:32-34