Numeri 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anauka pamaso pa Mose, pamodzi ndi amuna: mazana awiri mphambu makumi asanu a ana a Israyeli, ndiwo akalonga a khamulo, oitanidwa a msonkhano, amuna omveka.

Numeri 16

Numeri 16:1-9