Numeri 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Kora, mwana wa Izara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti, ana a Rubeni;

Numeri 16

Numeri 16:1-6