Numeri 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu amamka, nawaola, nawapera ndi mphero, kapena kuwasinja mumtondo, nawaphika m'mphika, nawaumba timitanda; ndi powalawa anali ngati timitanda tokazinga ndi mafuta.

Numeri 11

Numeri 11:1-18