Numeri 11:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyamayi ikali pakati pa mano, asanaitafune, Mulungu anapsa mtima pa anthuwa, ndipo Yehova anawakantha anthu ndi kukantha kwakukuru ndithu.

Numeri 11

Numeri 11:30-35