Numeri 11:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anauka tsiku lonselo, ndi usiku wace wonse, ndi mawa lace lonse, nakusa zinzirizo; wokusa pang'ono anakusa zodzaza mahomeri khumi; ndipo anadziyanikira izi pozungulira pa cigono.

Numeri 11

Numeri 11:25-35