Numeri 1:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero owerengedwa onse a ana a Israyeli monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akuturukira kunkhondo m'Israyeli;

Numeri 1

Numeri 1:39-53