Numeri 1:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo ndiwo amene anawerengedwa, amene Mose anawerenga pamodzi ndi Aroni, ndi akalonga a Israyeli, ndiwo amuna khumi ndi awiri; yense kunenera nyumba ya kholo lace.

Numeri 1

Numeri 1:37-51