Nehemiya 9:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munawapatsanso mzimu wanu wokoma kuwalangiza, ndipo simunawamana mana anu pakamwa pao; munawapatsanso madzi pa ludzu lao.

Nehemiya 9

Nehemiya 9:15-26