Nehemiya 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma Inu mwa nsoni zanu zazikuru simunawasiya m'cipululu; mtambo woti njo sunawacokera usana kuwatsogolera m'njira, ngakhale moto wa tolo usiku kuwaunikira panjira anayenera kuyendamo.

Nehemiya 9

Nehemiya 9:9-25