Nehemiya 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ninena nane mfumu, irikukhala pansi pamodzi ndi mkazi wace wamkuru, Ulendo wako ngwa nthawi yanji, udzabweranso liti? Ndipo kudakonda mfumu kunditumiza nditaichula nthawi.

Nehemiya 2

Nehemiya 2:2-10