Nehemiya 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinati kwa mfumu, Cikakomera mfumu, ndi mtima wanu ukakomera kapolo wanu, munditumize ku Yuda ku mudzi wa manda a makolo anga, kuti ndiumange.

Nehemiya 2

Nehemiya 2:1-11