Nehemiya 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Sanibalati Mhoroni, ndi Tobiya kapolo M-amoniyo, ndi Gesemu M-arabu, anamva natiseka pwepwete, natipeputsa, nati, Ciani ici mucicita? Mulikupandukira mfumu kodi?

Nehemiya 2

Nehemiya 2:18-20