Nehemiya 2:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinawauzanso za dzanja la Mulungu wanga londikhalira mokoma, ndiponso za mau anandiuza mfumu. Nati iwo, Tinyamuke, timange. Cotero anandilimbitsira manja mokoma.

Nehemiya 2

Nehemiya 2:17-20