Mlaliki 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mamawa fesa mbeu zako, madzulonso osapumitsa dzanja lako; pakuti sudziwa ziti zidzalola bwino ngakhale izizi, ngakhale izozo, kaya zonse ziwiri zidzakhala bwino.

Mlaliki 11

Mlaliki 11:3-10