Mlaliki 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga sudziwa njira ya mphepo, ngakhale makulidwe a mafupa m'mimba ya mkazi ali ndi pakati; momwemo sudziwa nchito za Mulungu amene acita zonse.

Mlaliki 11

Mlaliki 11:1-10