Miyambi 4:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Sinkasinkha bwino mayendedwe a mapazi ako;Njira zako zonse zikonzeke.

27. Usapatuke ku dzanja lamanja kapena kulamanzere;Suntha phazi lako kusiya zoipa.

Miyambi 4