Miyambi 3:33-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

33. Mulungu atemberera za m'nyumba ya woipa;Koma adalitsa mokhalamo olungama.

34. Anyozadi akunyoza,Koma apatsa akufatsa cisomo.

35. Anzeru adzalandira ulemu colowa cao;Koma opusa adzakweza manyazi.

Miyambi 3