Miyambi 22:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Ngati ulibe cobwezeraKodi acotserenji kama lako pansi pako?

28. Usasunthe cidziwitso cakale ca m'malire,Cimene makolo ako anaciimika.

29. Kodi upenya munthu wofulumiza nchito zace?Adzaima pamaso pa mafumu, osaima pamaso pa anthu acabe.

Miyambi 22