Miyambi 22:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi upenya munthu wofulumiza nchito zace?Adzaima pamaso pa mafumu, osaima pamaso pa anthu acabe.

Miyambi 22

Miyambi 22:25-29