Mika 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wokoma wa iwo akunga mitungwi; woongoka wao aipa koposa mpanda waminga; tsiku la alonda ako la kulangidwa kwako lafika, tsopano kwafika kuthedwa nzeru kwao.

Mika 7

Mika 7:1-9