Mika 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manja ao onse awiri agwira coipa kucicita ndi cangu; kalonga apempha, ndi woweruza aweruza cifukwa ca mphotho; ndi wamkuruyo angonena cosakaza moyo wace; ndipo aciluka pamodzi.

Mika 7

Mika 7:1-6