Mika 3:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova za aneneriakulakwitsa anthu anga; akuluma ndi mano ao, ndi kupfuula, Mtendere; ndipo, ali yense wosapereka m'kamwa mwao, amkonzera nkhondo;

Mika 3

Mika 3:4-12