Mateyu 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene Iye analowa m'nyumbamo, akhunguwo anadza kwa Iye; ndipo Yesu anati kwa iwo, Mukhulupirira kodi kuti ndikhoza kucita ici? Anena kwa Iye, Inde, Ambuye.

Mateyu 9

Mateyu 9:18-31