Mateyu 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ace;

2. ndipo anatsegula pakamwa, nawaphunzitsa iwo, nati:

Mateyu 5