Mateyu 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ace;

Mateyu 5

Mateyu 5:1-2