Mateyu 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Yesu anatengedwa ndi Mzimu kumka kucipululu kukayesedwa ndi mdierekezi.

2. Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pace anamva njala.

Mateyu 4