Mateyu 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anacoka msanga kumanda, ndi mantha ndi kukondwera kwakukuru, nathamanga kukauza ophunzira ace.

Mateyu 28

Mateyu 28:4-17