Mateyu 28:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pitani msanga, muuze ophunzira ace, kuti, Wauka kwa akufa; ndipo onani, akutsogolerani ku Galileya; mudzamuona Iye komweko; onani, ndakuuzani inu.

Mateyu 28

Mateyu 28:1-8