Mateyu 27:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Pilato poona kuti sanafitse, koma kuti linapambana phokoso, anatenga madzi, nasamba manja pamaso pa khamulo, nati, Ine ndiribe kucimwira mwazi wa munthu uyu wolungama, mudzionere nokha.

Mateyu 27

Mateyu 27:19-25