Mateyu 27:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onse anati, Apacikidwe pamtanda. Ndipo iye anati, Cifukwa ninji? anacita coipa cotani? Koma iwo anapfuulitsa kopambana, Apacikidwe pamtanda.

Mateyu 27

Mateyu 27:16-27